Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 5:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma ana ao amuna amene anawautsa m'malo mwao, iwowa Yoswa anawadula; popeza anakhala osadulidwa, pakuti sanawadula panjira.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 5

Onani Yoswa 5:7 nkhani