Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 5:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ana a Israyeli anayenda m'cipululu zaka makumi anai, mpaka mtundu wonse wa amuna ankhondo oturuka m'Aigupto udatha, cifukwa ca kusamvera mau a Yehova; ndiwo amene Yehova anawalumbirira kuti sadzawaonetsa dziko limene Yehova analumbirira makolo ao kudzatipatsa, ndilo dziko moyenda mkaka ndi uci.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 5

Onani Yoswa 5:6 nkhani