Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma m'mawa mwace mana analeka, atadya iwo tirigu wakhwimbi wa m'dziko; ndipo ana a Israyeli analibenso mana; koma anadya zipatso za dziko la Kanani caka comwe cija.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 5

Onani Yoswa 5:12 nkhani