Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 5:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo m'mawa mwace atatha Paskha, anadya tirigu wakhwimbi wa m'dziko, mikate yopanda cotupitsa ndi tirigu wokazinga tsiku lomwe lija.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 5

Onani Yoswa 5:11 nkhani