Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 24:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa ananena ndi anthu onse, Atero Yehova Mulungu wa Israyeli, Kale lija makolo anu anakhala tsidya lija la mtsinje, ndiye Tera, atate wa Abrahamu ndi atate wa Nahori; natumikira milungu yina iwowa.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:2 nkhani