Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 24:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anasonkhanitsa mapfuko onse a Israyeli ku Sekemu, naitana akulu akulu a Israyeli ndi akuru ao, ndi oweruza ao, ndi akapitao ao; ndipo anadzilangiza pamaso pa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 24

Onani Yoswa 24:1 nkhani