Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 23:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo taonani, lero lino ndirikumuka njira ya dziko lonse lapansi; ndipo mudziwa m'mitima yanu yonse, ndi m'moyo mwa inu nonse, kuti pa mau okoma onse Yehova Mulungu wanu anawanena za inu sanagwa padera mau amodzi; onse anacitikira inu, sanasowapo mau amodzi.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 23

Onani Yoswa 23:14 nkhani