Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Pinehasi wansembe, ndi akalonga a msonkhano ndi akuru a mabanja a Israyeli okhala naye anamva mau adawanena ana a Rubeni, ndi ana a Gadi, ndi ana a Manase, anawakomera pamaso pao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:30 nkhani