Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Sikungatheke kuti tipikisane ndi Yehova ndi kubwerera lero kusatsata Yehova, kumanga guwa la nsembe la kufukizapo nsembe yopsereza, la nsembe yaufa, kapena yophera, pamodzi ndi guwa la nsembe la Yehova Mulungu wathu lokhala pakhomo pa cihema cace.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:29 nkhani