Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace tinati, Kudzali, akadzatero kwa ife, kapena kwa mibadwo yathu m'tsogolomo, kuti tidzati, Tapenyani, citsanzo ca guwa la nsembe la Yehova, comanga makolo athu, si kufukizapo nsembe yopsereza ai, kapena nsembe yophera ai, koma ndilo mboni pakati pa ife ndi inu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:28 nkhani