Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma lidzakhala mboni pakati pa ife ndi inu; ndi pakati pa mibadwo yathu ya m'tsogolo, kuti tikacita nchito ya Yehova pamaso pace ndi nsembe zathu zopsereza, ndi zophera, ndi zoyamika; kuti ana anu asanene ndi ana athu m'tsogolomo, Mulibe gawo ndi Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:27 nkhani