Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 22:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anafikira mbali ya ku Yordano, ndilo la m'dziko la Kanani, ana a Rubeni, ndi ana a Gadi, ndi pfuko la Manase logawika pakati anamanga ku Yordano guwa la nsembe, guwa lalikuru maonekedwe ace.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 22

Onani Yoswa 22:10 nkhani