Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 18:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Alevi alibe gawo pakati pa inu; pakuti unsembe wa Yehova ndiwo colowa cao. Koma Gadi, ndi Rubeni, ndi pfuko la Manase logawika pakati adalandira colowa cao tsidya lija la Yordano kum'mawa, cimene Mose mtumiki wa Yehova adawapatsa.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 18

Onani Yoswa 18:7 nkhani