Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 18:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo muzilemba dziko likhale magawo asanu ndi awiri, ndi kubwera nao kuno kwa ine malembo ace; ndipo ndidzakuloterani maere pane pamaso pa Yehova Mulungu wathu.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 18

Onani Yoswa 18:6 nkhani