Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 16:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo gawo La ana a Yosefe linaturuka kucokera ku Yordano ku Yeriko, ku madzi a Yeriko kum'mawa, kucipululu, nakwera kucokera ku Yeriko kumka kumapiri ku Beteli;

Werengani mutu wathunthu Yoswa 16

Onani Yoswa 16:1 nkhani