Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 11:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti cidadzera kwa Yehova kulimbitsa mitima yao kuti athirane nao Aisrayeli nkhondo kuti iye awaononge konse, kuti asawacitire cifundo koma awaononge, monga Yehova adalamulira Mose.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 11

Onani Yoswa 11:20 nkhani