Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 11:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yoswa anadza nthawi yomweyo, napasula Aanaki kuwacotsa kumapiri, ku Hebroni, ku Dibiri, ku Anabi, ndi ku mapiri onse a Yuda, ndi ku mapiri onse a Israyeli; Yoswa anawaononga konse, ndi midzi yao yomwe.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 11

Onani Yoswa 11:21 nkhani