Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, ataturutsira Yoswa mafumu awa, Yoswa anaitana amuna onse a Israyeli, ndipo anati kwa akazembe a anthu a nkhondo amene anamuka naye, Yandikirani, pondani pa makosi a mafumu awa. Nayandikira iwo, naponda pa makosi ao.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:24 nkhani