Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yoswa 10:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Yoswa ananena nao, Musaope, musatenge nkhawa; khalani amphamvu, nimulimbike mtima; pakuti Yehova adzatero ndi adani: anu onse amene mugwirana nao: nkhondo.

Werengani mutu wathunthu Yoswa 10

Onani Yoswa 10:25 nkhani