Mulekeranji kukhululukira kulakwa kwanga ndi kundicotsera mphulupulu yanga?Popeza tsopano ndidzagona kupfumbi;Mudzandifunafuna, koma ine palibe.