Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yobu 7:19-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

19. Mukana kundicokera kufikira liti,Kapena kundileka mpaka nditameza dobvu?

20. Ngati ndacimwa, ndingacitire Inu ciani, Inu wodikira anthu?Mwandiikiranji ndikhale candamali canu?Kuti ndikhale kwa ine ndekha katundu?

21. Mulekeranji kukhululukira kulakwa kwanga ndi kundicotsera mphulupulu yanga?Popeza tsopano ndidzagona kupfumbi;Mudzandifunafuna, koma ine palibe.

Werengani mutu wathunthu Yobu 7