Ngati ndacimwa, ndingacitire Inu ciani, Inu wodikira anthu?Mwandiikiranji ndikhale candamali canu?Kuti ndikhale kwa ine ndekha katundu?