Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 66:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo iwo adzatenga abale anu onse mwa amitundu onse akhale nsembe ya kwa Yehova; adzabwera nao pa akavalo, ndi m'magareta, ndi m'macila, ndi pa nyuru, ndi pa ngamila, kudza ku phiri langa lopatulika ku Yerusalemu, ati Yehova, monga ana a Israyeli abwera nazo nsembe zao m'cotengera cokonzeka ku nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:20 nkhani