Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 66:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ndidzaika cizindikiro pakati pao, ndipo ndidzatumiza onse amene apulumuka mwa iwo kwa amitundu, kwa Tarisi, kwa Puli ndi kwa Aludi, okoka uta kwa Tubali ndi Yavana, ku zisumbu zakutari, amene sanamve mbiri yanga, ngakhale kuona ulemerero wanga; ndipo adzabukitsa ulemerero wanga pakati pa amitundu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 66

Onani Yesaya 66:19 nkhani