Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 62:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti monga mnyamata akwatira namwali, momwemo ana ako amuna adzakukwama iwe; ndi monga mkwati akondwera ndi mkwatibwi, momwemo Mulungu wako adzakondwera nawe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 62

Onani Yesaya 62:5 nkhani