Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 53:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti ameneyo adzaphuka pamaso pace ngati mtengo wanthete, ndi ngati muzu womera m'nthaka youma; Iye alibe maonekedwe, pena kukongola; ndipo pamene timuona palibe kukongola kuti timkhumbe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 53

Onani Yesaya 53:2 nkhani