Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 52:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ha, akongolatu pamapiri mapazi a iye amene adza ndi uthenga wabwino, amene abukitsa mtendere, amene adza ndi uthenga wabwino wa zinthu zabwino, amene abukitsa cipulumutso; amene ati kwa Ziyoni, Mulungu wako ndi mfumu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 52

Onani Yesaya 52:7 nkhani