Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 52:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Galamuka galamuka, tabvala mphamvu zako, Ziyoni; tabvala zobvala zako zokongola, Yerusalemu, mzinda wopatulika; pakuti kuyambira tsopano sadzalowanso kwa iwe wosadulidwa ndi wodetsedwa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 52

Onani Yesaya 52:1 nkhani