Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 50:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa canji ndinafika osapeza munthu? ndi kuitana koma panalibe wina woyankha? Kodi dzanja langa lafupika konse, kuti silingathe kuombola? pena Ine kodi ndilibe mphamvu zakupulumutsa? Taona pa kudzudzula kwanga ndiumitsa nyanja yaikuru, ndi kusandutsa mitsinje cipululu; nsomba zace zinunkha cifukwa mulibe madzi, nizifa ndi ludzu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 50

Onani Yesaya 50:2 nkhani