Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 50:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Kalata wa cilekaniro ca amako ali kuti amene ndinamsudzula naye? pena ndani wa angongole anga amene ndamgulitsa iwe? Taona cifukwa ca zoipa zanu munagulitsidwa, ndi cifukwa ca kulakwa kwanu amanu anacotsedwa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 50

Onani Yesaya 50:1 nkhani