Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 50:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani ali mwa inu amene amaopa Yehova, amene amamvera mau a mtumiki wace? Iye amene ayenda mumdima, ndipo alibe kuunika, akhulupirire dzina la Yehova, ndi kutsamira Mulungu wace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 50

Onani Yesaya 50:10 nkhani