Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 50:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taonani, inu nonse amene muyatsa moto, amene mudzimangira m'cuuno ndi nsakali, yendani inu m'cirangati ca moto wanu, ndi pakati pa nsakali zimene mwaziyatsa. Ici mudzakhala naco ca pa dzanja langa; mudzagona pansi ndi cisoni.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 50

Onani Yesaya 50:11 nkhani