Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Mombolo wa Israyeli, ndi Woyera wace, kwa Iye amene anthu amnyoza, kwa Iye amene mtundu wathu unyansidwa naye, kwa mtumiki wa olamulira: Mafumu adzaona, nadzauka; akalonga nadzalambira cifukwa ca Yehova, amene ali wokhulupirika, ngakhale Woyera wa Israyeli, amene anakusankha Iwe.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:7 nkhani