Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

inde, ati, Ciri cinthu copepuka ndithu kuti Iwe ukhale mtumiki wanga wakuutsa mafuko a Yakobo, ndi kubwezera osungika a Israyeli; ndidzakupatsanso ukhale kuunika kwa amitundu, kuti ukhale cipulumutso canga mpaka ku malekezero a dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:6 nkhani