Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Nthawi yondikomera ndakuyankha Iwe, ndi tsiku la cipulumutso ndakuthandiza; ndipo ndidzakusunga ndi kupatsa Iwe ukhale pangano la anthu, kuti ukhazikitse dziko, nuwalowetse m'zolowa zopasuka m'malo abwinja;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:8 nkhani