Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsopano, ati Yehova, amene anandiumba Ine ndisanabadwe ndikhale mtumiki wace, kubwezanso Yakobo kwa Iye, ndi kuti Israyeli asonkhanidwe kwa Iye; cifukwa Ine ndiri wolemekezeka pamaso pa Yehova, ndipo Mulungu wanga wakhala mphamvu zanga;

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:5 nkhani