Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Ambuye Yehova, Taona ndidzakodola anthu a mitundu, ndi kukwezera anthu mbendera yanga; ndipo adzabwera nao ana ako amuna pa cifuwa cao, ndi ana ako akazi adzatengedwa pa mapewa ao.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:22 nkhani