Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo udzati m'mtima mwako, Ndani wandibalitsa ine amenewa, popeza ana anga anacotsedwa kwa ine, ndipo ndiri wouma, ndi wocotsedwa m'dziko, ndi woyendayenda kwina ndi kwina? ndipo ndani wadza ndi awa? Taona ndinasiyidwa ndekha, amenewa anali kuti?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:21 nkhani