Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 49:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mafumu adzakulera, ndi akazi ao akuru adzakuyamwitsa; iwo adzakugwadira ndi nkhope zao zoyang'ana pansi, nadzaseteka pfumbi la m'mapazi ako: ndipo iwe udzadziwa kuti Ine ndine Yehova, ndi iwo amene alindira Ine sadzakhala ndi manyazi.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 49

Onani Yesaya 49:23 nkhani