Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 45:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nenani inu, turutsani mlandu wanu; inde, acite uphungu pamodzi; ndani waonetsa ici ciyambire nthawi yakale? ndani wanena ici kale? kodi si ndine Yehova? ndipo palibenso Mulungu wina popanda Ine; Mulungu wolungama, ndi Mpulumutsi; palibenso wina popanda Ine.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 45

Onani Yesaya 45:21 nkhani