Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 45:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ine ndautsa Koresi m'cilungamo, ndipo ndidzalungamitsa njira zace zonse; iye adzamanga mudzi wanga, nadzaleka andende anga anke mwa ufulu, wosati ndi mtengo pena mphotho, ati Yehova wa makamu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 45

Onani Yesaya 45:13 nkhani