Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 45:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Nchito ya Aigupto, ndi malonda a Kusi, ndi a Sabea, amuna amsinkhu adzakugonjera, nadzakhala ako; nadzakutsata pambuyo m'maunyolo; adzakugonjera, nadzakugwira; adzakupembedza ndi kunena, Zoona Mulungu ali mwa iwe; ndipo palibenso wina, palibe Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 45

Onani Yesaya 45:14 nkhani