Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova, Mombolo wako, ndi Iye amene anakuumba iwe m'mimba, Ine ndine Yehova, amene ndipanga zinthu zonse, ndi kufunyulula ndekha zakumwamba, ndi kuyala dziko lopansi; ndani ali ndi Ine?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:24 nkhani