Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Yimbani m'mwamba inu, pakuti Yehova wacicita ico; kuwani inu, mbali za pansi pa dziko; yimbani mapiri inu; nkhalango iwe, ndi mitengo yonse m'menemo; cifukwa kuti Yehova wapulumutsa Yakobo, ndipo adzadzilemekezetsa yekha mwa Israyeli.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:23 nkhani