Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Iye adzidulira yekha mikungudza, natenga mtengo wambawa, ndi wathundu, ndi kudzisankhira yekha wina wa mitengo ya nkhalango; naoka mtengo wamlombwa, mvula niukulitsa.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:14 nkhani