Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Mmisiri wa mitengo atambalitsa cingwe; nalilemba ndi colembera, nalikonza ndi ncerero, nalilemba ndi zolinganizira, nalifanizira monga maonekedwe a munthu, monga munthu wokongola, kuti likhale m'nyumba.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:13 nkhani