Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 44:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo udzakhala kuti munthu autenthe; iye natengako, nauotha moto; inde auyatsa, naoca mkate; inde, apanga mlungu, naulambira, naupanga fano losema, naligwadira.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 44

Onani Yesaya 44:15 nkhani