Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 42:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndani anapereka Yakobo, kuti afunkhidwe, ndi Israyeli, kuti awawanyidwe? kodi si Yehova? Iye amene tamcimwira, ndi amene iwo anakonda kuyenda m'njira zace, ngakhale kumvera ciphunzitso cace.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 42

Onani Yesaya 42:24 nkhani