Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 36:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma kazembeyo anati, Kodi mbuyanga ananditumiza ine kwa mbuyako ndi kwa iwe kunena mau amenewa? kodi iye sananditumiza ine kwa amuna okhala palinga, kuti adye ndowe zao zao, ndi kumwa madzi ao ao ndi inu?

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:12 nkhani