Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yesaya 36:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eliakimu, ndi Sebina, ndi Yoaki, anati kwa kazembeyo, Nenanitu kwa atumiki anu m'cinenero ca Aramu; pakuti ife ticimva; ndipo musanene kwa ife m'Ciyuda, m'makutu a anthu amene ali palinga.

Werengani mutu wathunthu Yesaya 36

Onani Yesaya 36:11 nkhani